Kudziwa Zambiri za Msonkho

Featured Impact Stories

Mabuku Okhudza Zachuma samakamba mozama nkhani zikhudza misonkho.mabukwa amatenga msonkho ngati chinthu chomwe chimagwiritsidwa ntchito pa ntchito yoyendetsa chuma, pogawa chuma cha m’dziko kapena posintha mchitidwe wa nthu (Monga pofuna kuwalimbikitsakuti achepetse mchitidwe wawo woononga chilengedwe)


View and download the book from the here